News

AMUMASULA PA MILANDU OGWILILIRA

Mtolankhani wanthu

Bambo wina, Gift Mlenga wamasulidwa ndi bwalo la milandu ku Mulanje, apolisi atamumanga sabata zingapo zapitazo pomuganizira kuti anagwililira mwana wake omupeza wa zaka 13.

Oweluza ku bwalo la Senior Resident Magistrate m’bomalo, Shaheeda Bakili wati mbali ya boma pa mlanduwu inalibe umboni okwanira otsimikizira za nkhaniyi.

Mlenga yemwe ndi ogwira ntchito ku bungwe logulitsa ndi kugawa magetsi la ESCOM anamangidwa pa 26 May chaka chino.

Pa nthawiyo, zidamveka kuti Mlenga adakhala akumugona mwanayu kuchokera mu 2014 pomwe adalowa banja ndi mai ake ndipo akuti ankamuopseza kuti amupha akawulula.

Team Plus TV

We are a digital TV station that videocast live events and news as it come into being which we publish across all formats biginning with this platform, we hope to appeal to the bulk of young and middle class elites with a vision of the future and belief in a social change. Pin on delivering fresh , factual and reliable news . We offer the fastest and deepest journalism, it is one stop media portal with high standards in content creation. Our primary value is our audience thus creating relevant content that matters.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *