NationalNews

CHAKA KU NDENDE ATAVULAZA GALU

Mtolankhani wanthu

Bambo wa zaka 42, Lameck Mkandawire wa ku Engalaweni m’boma la Mzimba amugamula kukakhala ku ndende kwa chaka chimodzi pa mlandu ovulaza galu.

Malipoti akuti mwini galuyo anawuza apolisi kuti anapeza a Mkandawire akumenya galuyo m’mutu.

Apa ndi pomwe apolisi anatsegulira mkuluyu mlandu omwe mboni ya boma, Happy Mlera anati a Mkandawire amamenya galuyo ali omangililidwa pa tcheni.

Oweruza mulanduwu, Wongani Kumwenda anapeza Mkandawire olakwa ndi kumupatsa chilango chotere.

Team Plus TV

We are a digital TV station that videocast live events and news as it come into being which we publish across all formats biginning with this platform, we hope to appeal to the bulk of young and middle class elites with a vision of the future and belief in a social change. Pin on delivering fresh , factual and reliable news . We offer the fastest and deepest journalism, it is one stop media portal with high standards in content creation. Our primary value is our audience thus creating relevant content that matters.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *